Mawu a M'munsi
d Anthu amakhulupirira kuti Uthenga Wabwino wa Mateyo unalembedwa m’Chiheberi ndi mtumwi Mateyo. Ngakhale zitakhala kuti ndi zoona, uthenga umene ulipo mpaka pano ndi wa m’Chigiriki, ndipo n’kutheka kuti Mateyo yemweyo ndi amene anamasulira.