Mawu a M'munsi
a M’zikhalidwe zina, anthu amaona kuti ndi mwano kuitana munthu wachikulire pomutchula dzina lake loyamba, pokhapokha ngati munthu wachikulireyo atanena kuti palibe vuto kutero. Akhristu ayenera kulemekeza zikhalidwe zoterozo.