Mawu a M'munsi
a Zikuoneka kuti mabuku ouziridwa omwe Yoswa anali nawo panthawiyo anali mabuku asanu olembedwa ndi Mose (Genesis, Eksodo, Levitiko, Numeri ndi Deuteronomo), buku la Yobu ndiponso Salmo limodzi kapena awiri.