Mawu a M'munsi
a Taonani ena mwa malonjezo amene Yoswa anaona akukwaniritsidwa. Yehova adzapatsa Aisiraeli dziko lawolawo. (Yerekezerani Genesis 12:7 ndi Yoswa 11:23.) Yehova adzalanditsa Aisiraeli m’dziko la Iguputo. (Yerekezerani Eksodo 3:8 ndi Eksodo 12:29-32.) Yehova adzasamalira anthu ake.—Yerekezerani Eksodo 16:4, 13-15 ndi Deuteronomo 8:3, 4.