Mawu a M'munsi
b Anthu a ku Kanani ankaona kuti Baala ndiye anali mulungu wamkulu kwambiri, ndipo Asitaroti anali mulungu wamkazi amene anthuwa ankakhulupirira kuti anali mkazi wa Baala.