Mawu a M'munsi
b M’fanizo limeneli kufesa sikukutanthauza ntchito yolalikira ndi kupanga ophunzira imene imathandiza kuti anthu atsopano akhale Akhristu odzozedwa. Ponena za mbewu zabwino zimene zinafesedwa m’munda Yesu anati: Mbewuzi “ndi ana a ufumu.” Iye sanati “adzakhala” ana a ufumu. Choncho, kufesa kukutanthauza kudzoza ana a Ufumuwo padziko lapansi.