Mawu a M'munsi
b Mateyo analemba kuti alendo amenewa “anamasula chuma chawo” ndipo anam’patsa Yesu golide, lubani ndi mule. N’zochititsa chidwi kuti mphatso zamtengo wapatali zimenezi zinafika panthawi yake, popeza zikuoneka kuti makolo a Yesu anali osauka ndiponso chifukwa choti anali atatsala pang’ono kuthawira kudziko lina.—Mateyo 2:11-15.