Mawu a M'munsi
d Maganizo amenewa, omwe anayambitsidwa ndi Jerome cha m’ma 383 C.E., ndi otchuka kwambiri kwa anthu amene amakhulupirira kuti Mariya anakhala namwali kwa moyo wake wonse. Patapita nthawi Jerome anazindikira kuti maganizo akewa ndi olakwika. Koma anthu ambiri, makamaka akuluakulu a tchalitchi cha Katolika amakhulupirirabe zimenezi.