Mawu a M'munsi
a Akatswiri ena amatsutsa zoti zilembo zimenezi zimasonyeza kuti Ashasu “anali anthu otsatira mulungu wotchedwa Yahweh.” Iwo amaona kuti dzina la dziko limeneli silodziwika, motero ngakhale kuti n’lofanana ndi dzina la Mulungu wa Aisiraeli, zimenezi zinangochitika koma palibe mgwirizano uliwonse.