Mawu a M'munsi
a Baibulo la New World Translation, limafalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Baibulo limeneli lilipo m’Chichewa kuyambira Mateyo mpaka Chivumbulutso, ndipo limatchedwa Baibulo la Dziko Latsopano Lomasulira Malemba Achigiriki Achikhristu. Padziko lonse, Baibulo la New World Translation limapezeka lonse kapena mbali yake chabe m’zilankhulo 83. Baibulo limeneli likupezekanso pa Intaneti m’zinenero 17 pa adiresi iyi: www.pr2711.com.