Mawu a M'munsi
a Yerobiamu anayambitsa kulambira fano la mwana wang’ombe mu ufumu wakumpoto wa Isiraeli wa mafuko khumi. Iye anachita zimenezi n’cholinga choti anthu asiye kupita ku Yerusalemu kukalambira Yehova.