Mawu a M'munsi a Mabaibulo ena pa lembali amati: “Um’tumikire ndi mtima wonse komanso mwakufuna kwako.”