Mawu a M'munsi
b Ngati mukufuna kudziwa mfundo zokuthandizani kuyamba kukambirana ndi mwana wanu nkhani zokhudza kugonana komanso zimene mungakambirane naye malinga ndi msinkhu wake, werengani Nsanja ya Olonda ya November 1, 2010, tsamba 12 mpaka 14.