Mawu a M'munsi
a N’zochititsa manyazi kuti Matchalitchi Achikhristu amagwiritsa ntchito nkhani za m’Mauthenga Abwino, zonena za kuphedwa kwa Yesu, polimbikitsa anthu kuti azidana ndi Ayuda. Koma amene analemba Uthenga Wabwino, amenenso anali Ayuda, analibe maganizo amenewo.