Mawu a M'munsi
b Munthu ankaonedwa kuti wanyoza Mulungu ngati wachita chilichonse chosonyeza kusalemekeza dzina la Mulungu kapena ngati akufuna kulanda mphamvu komanso udindo umene Mulungu yekha ndi amene ayenera kukhala nawo. Anthu amene ankaimba Yesu mlandu analephera kupereka umboni wosonyeza kuti anapalamula milandu imeneyi.