Mawu a M'munsi
a Buku lina la Akatolika limanena kuti ulosi umenewu unkatanthauza kuti: “Pa nthawi imene Yerusalemu azidzawonongedwa, anthu ambiri a mumzindawu adzaphedwa ndipo mitembo yawo siidzaikidwa m’manda koma idzangotayidwa m’chigwa kuti iwole kapena kupsa.”—New Catholic Encyclopedia.