Mawu a M'munsi
c Buku lina linanena kuti mawu achiheberi amene pa Genesis 2:24 anawamasulira kuti “kudziphatika” angatanthauze ‘kusafuna kusiya munthu winawake chifukwa chomukonda ndiponso kufuna kukhalabe wokhulupirika kwa iye.’