Mawu a M'munsi
a M’Mabaibulo ena palembali pamati: “AMBUYE ndi M’busa wanga.” Kuti mudziwe chifukwa chake Mabaibulo ena anachotsa dzina la Mulungu lakuti Yehova, werengani tsamba 195 mpaka 197 m’buku la Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.