Mawu a M'munsi c Izi zinachitika pambuyo poti Ayuda enieni apatsidwa mpata wa zaka zitatu ndi hafu woti akhale mbali ya mtundu wauzimu watsopano. Zimene zinachitikazi zinatchulidwa mu ulosi wa milungu 70 ya zaka.—Dan. 9:27.