Mawu a M'munsi
b N’zochititsa chidwi kuti Baibulo limanena kuti dziko lapansi ndi lozungulira. Aristotle ndiponso anthu ena akale a ku Greece anapezanso kuti dziko lapansi ndi lozungulira. Koma panatenga zaka zambirimbiri kuti asayansi ena aivomereze mfundo imeneyi.