Mawu a M'munsi
d N’kutheka kuti “gulu la nyenyezi la Kima” likutanthauza gulu la nyenyezi lotchedwa Nsangwe [m’Chingelezi, Pleiades]. “Gulu la nyenyezi la Kesili” liyenera kuti limaimira gulu la nyenyezi lotchedwa Akamwiniatsatana [m’Chingelezi, Orion]. Pamatenga zaka masauzande ambiri kuti magulu amenewa a nyenyezi asinthe kwambiri.