Mawu a M'munsi
e Chifukwa choti Mulungu anagwiritsira ntchito Mwana wake wauzimu wobadwa yekha ngati “mmisiri waluso” kuti alenge zinthu zonse, mawu amene ali palembali angagwirenso ntchito kwa Mwana wakeyu.—Miyambo 8:30, 31; Akolose 1:15-17; Aheberi 1:10.