Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

f M’zaka za m’ma 1800, wasayansi wina dzina lake William Thomson, amene amadziwikanso kuti Lord Kelvin, anatulukira lamulo lachiwiri lokhudza mphamvu yopezeka m’zinthu zachilengedwe. Lamuloli limafotokoza zimene zimachititsa kuti pakapita nthawi, zinthu zachilengedwe ziziwonongeka ndiponso kutha. Chimodzi mwa zinthu zimene zinamuthandiza kuti apeze zimenezi, ndi choti anaphunzira mosamala tanthauzo la mawu a pa Salimo 102:25-27.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena