Mawu a M'munsi
b Nyuzipepala ina inati: “Lamuloli linakhazikitsidwa pomvera zimene a Tchalitchi cha Orthodox ku Russia ananena. Iwo ankafuna kukhalabe chipembedzo chachikulu ku Russia choncho ankafuna kwambiri kuti boma litseke chipembedzo cha Mboni za Yehova.”—Associated Press, June 25, 1999.