Mawu a M'munsi
e Pa NovemberĀ 22, 2010, oweruza 5 omwe ndi akuluakulu a khotili anakana pempho la boma la Russia lakuti iwo aweruzenso mlanduwu. Izi zinachititsa kuti chigamulo chimene chinaperekedwa pa JuneĀ 10, 2010, chikhale chomaliza ndiponso chitsatiridwe.