Mawu a M'munsi
a Ansembe ndi Alevi ankagwira ntchito tsiku la Sabata pakachisi koma ‘ankakhalabe osalakwa.’ Popeza Yesu ndi mkulu wa ansembe wa kachisi wamkulu wauzimu wa Mulungu, iye akanatha kugwira ntchito yake yauzimu osaopa kuti akuphwanya lamulo la Sabata.—Mat. 12:5, 6.