Mawu a M'munsi
c Munthu amene ankagwira ntchito kunyumba kwa Mfumu Sauli, yemwe anauza mfumuyo za Davide, ananenanso kuti Davideyo anali “wolankhula mwanzeru ndi wooneka bwino, komanso Yehova [anali] naye.”—1 Samueli 16:18.