Mawu a M'munsi
a Mabuku awa ofalitsidwa ndi Mboni za Yehova angathandize makolo pophunzitsa ana awo nkhani zimenezi: Galamukani! ya May 2006, tsamba 10-13, m’nkhani yakuti, “Thandizani Mwana Wanu Wamkazi Kukonzekera Kutha Msinkhu.” Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, m’mutu 6 wakuti, “Kodi Thupi Langali Latani?” Komanso Nsanja ya Olonda ya November 1, 2010, tsamba 12-14 m’nkhani yakuti, “Chinsinsi cha Banja Losangalala—Muzikambirana ndi Ana Anu Nkhani Zokhudza Kugonana.”