Mawu a M'munsi
a Buku la Insight on the Scriptures limafotokoza kuti: “Kale munthu akakhala maso koma n’kuona masomphenya ochokera kwa Mulungu, zikuoneka kuti masomphenyawo ankakhazikika m’maganizo ndi mumtima mwake. Kenako munthuyo ankatha kukumbukira masomphenyawo n’kuwalemba kapena kuwafotokoza m’mawu akeake.”—Lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.