Mawu a M'munsi
b Kuphedwa kwa anthu ambiri pa nthawi ya ulamuliro wa chipani cha Nazi ku Germany, ndi chitsanzo cha zimene boma lina linachita pofuna kuthetsa zipembedzo komanso mitundu ina ya anthu. M’nthawi ya ulamuliro wa Soviet Union, magulu azipembedzo omwe anali m’dzikolo ankachitiridwa nkhanza zoopsa. Onani nkhani yakuti, “Anthu Okonda Mtendere Akuyesetsa Kuti Anthu Asaipitse Mbiri Yawo,” mu Nsanja ya Olonda ya May 1, 2011, yofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.