Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe zambiri pa nkhani yakuti Mulungu aliko, onani kabuku kachingelezi kakuti The Origin of LifeāFive Questions Worth Asking komanso buku lachingelezi lakuti Is There a Creator Who Cares About You? Mabuku amenewa ndi ofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.