Mawu a M'munsi
a A Mboni za Yehova ndi okonzeka kukuthandizani kuphunzira choonadi chonena za Mulungu komanso zimene iye akufuna kuchita. Iwo amaphunzira Baibulo ndi anthu kwaulere pogwiritsa ntchito buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?