Mawu a M'munsi
a Koma sikuti tizigwiritsa ntchito malangizo a m’Baibulo pokakamiza ena kuchita zinazake kapena powasonyeza kuti iwo ndi oipa. Tiyenera kukhala oleza mtima ndiponso kukomera mtima anthu amene tikuphunzira nawo Baibulo ngati mmene Yehova amachitira ndi ifeyo.—Sal. 103:8.