Mawu a M'munsi
b Kodi mungatani ngati mukukumbukira mawu enaake a m’Baibulo koma mwaiwala buku, chaputala ndi vesi? Mwina mukhoza kupeza lembalo mutafufuza mawuwo mu kalozera wa mawu a m’Baibulo kumapeto kwa Baibulo la Dziko Latsopano kapena mu Watchtower Library.