Mawu a M'munsi
c Makalata a Paulo ali ndi malangizo othandiza kwambiri polimbana ndi kupanda ungwiro. (Aroma 6:12; Agal. 5:16-18) Iyenso ayenera kuti ankatsatira malangizo amene ankapereka kwa anthu ena.—Aroma 2:21.