Mawu a M'munsi
b Kuti mudziwe zambiri pankhaniyi, mungaone nkhani zoyambirira za m’magazini ya Galamukani! ya April 2012, yomwe ili ndi mutu wakuti, “Kodi Mabanja Amene Ali ndi Ana Opeza Angatani Kuti Zinthu Ziziwayendera?” yofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.