Mawu a M'munsi
a Akatswiri ambiri amavomereza kuti malinga ndi Chilamulo, munthu wopalamula milandu ikuluikulu ankaphedwa kaye kenako n’kupachika thupi lake. Koma pali umboni wakuti m’nthawi ya atumwi, Ayuda ankapachika anthu ena ali moyo moti ankafera pamtengo pompo.