Mawu a M'munsi a Patapita nthawi, bambo anga, mayi anga, mchemwali wanga wamkulu komanso ang’ono anga awiri anakhalanso a Mboni.