Mawu a M'munsi
a Ndime 3: Nthawi ina Yesu anadyetsanso mozizwitsa amuna 4,000 limodzi ndi akazi ndi ana. Iye anatenganso chakudya “n’kupatsa ophunzirawo ndipo iwo anagawira khamu la anthulo.”—Mat. 15:32-38.