Mawu a M'munsi
c Ndime 8: Mawu akuti Akhristu atsopano “anapitiriza kulabadira zimene atumwiwo anali kuphunzitsa” akusonyeza kuti atumwi ankaphunzitsa anthu nthawi zonse. Zinthu zina zimene atumwi ankaphunzitsa zinalembedwa m’mabuku a Malemba Achigiriki.