Mawu a M'munsi
e Ndime 13: Mawu a mtumwi Paulo pa lemba la Machitidwe 20:29, 30 anasonyeza kuti mpingo udzasokonezedwa ndi anthu ochokera mbali ziwiri. Poyamba, ananena kuti Akhristu onyenga (“namsongole”) ‘adzafika pakati pa’ Akhristu oona. Kenako ananena kuti ‘pakati pa’ Akhristu oonawo, ena adzapatuka n’kuyamba kulankhula “zinthu zopotoka.”