Mawu a M'munsi
a Ndime 2: [1] Pa nthawi ina, Yesu anali atanena fanizo lofanana ndi limeneli. M’fanizolo, anagwiritsa ntchito mawu oti “mtumiki woyang’anira nyumba” ponena za “kapolo” ndiponso mawu oti “gulu la atumiki ake” ponena za “antchito ake apakhomo.”—Luka 12:42-44.