Mawu a M'munsi
b Ndime 6: [2] Ponena za Khristu, mawu achigiriki amene anawamasulira kuti ‘kubwera’ (erʹkho·mai) ndi osiyana ndi amene anawamasulira kuti “kukhalapo” (pa·rou·siʹa). Kukhalapo kwake kunayamba kale koma adzabwera kudzaweruza m’tsogolo.