Mawu a M'munsi
a Mawu achiheberi amene anawamasulira kuti “mtsikana” pa Yesaya 7:14 angatanthauze mkazi wokwatiwa komanso namwali. Choncho mawuwa akhoza kugwiritsidwa ntchito ponena za mkazi wa Yesaya komanso Mariya, pa nthawi imene anali namwali.