Mawu a M'munsi
a Nyamakaziyi nthawi zambiri imagwira ana. Zimene zimachitika ndi zoti, chitetezo cha m’thupi chimaukira mtundu winawake wa maselo ndipo izi zimachititsa kuti munthu azimva kupweteka m’malo olumikizirana mafupa komanso kuti malowa azitupa.