Mawu a M'munsi
a Pofotokoza mawu a Mulungu a pa Ekisodo 3:14, katswiri wina analemba kuti: “Palibe chimene chingamulepheretse kuchita zimene akufuna . . . Dzina limeneli [lakuti Yehova] linali ngati mpanda wolimba wa Aisiraeli ndipo likanawathandiza kukhala ndi chiyembekezo komanso kuti asamade nkhawa.”