Mawu a M'munsi
d Malipoti ochokera mâmayiko osiyanasiyana akusonyeza kuti munthu akasiyana ndi banja lake pamakhala mavuto ambiri. Ena amachita chigololo, amagonana ndi amuna kapena akazi anzawo kapenanso ndi achibale awo.Ana amalowerera, sakhoza bwino kusukulu, amakhala olusa, ankhawa ndiponso mwina amafuna kudzipha.