Mawu a M'munsi
c Mmishonale wina, dzina lake John Hunt, ndi amene anamasulira mbali yaikulu ya Chipangano Chatsopano m’Chifiji. Baibulo lomwe anamasuliralo linasindikizidwa mu 1847. Baibuloli ndi lofunika kwambiri chifukwa mumapezeka dzina la Mulungu lakuti, “Yehova” pa Maliko 12:36, Luka 20:42 ndi pa Machitidwe 2:34.