Mawu a M'munsi
a Anthu a ku Filipi ankalamuliridwa ndi Aroma. Ndiyeno mwina anthu ena mumpingo anali nzika za Roma. Choncho iwo ankakhala ndi ufulu wina umene Akhristu anzawo analibe.