Mawu a M'munsi
b Onaninso mbiri ya moyo wa Hadyn ndi Melody Sanderson m’nkhani yakuti, “Kudziwa ndi Kuchita Chabwino” ya mu Nsanja ya Olonda ya March 1, 2006. Iwo anasiya bizinezi yawo ya ndalama zambiri ku Australia n’kuyamba utumiki wa nthawi zonse. Werengani zimene zinachitika ndalama zitawathera pamene ankachita umishonale ku India.